|
Anti Ahmadiyya Movement in Islam
CHIPEMBEZO NDI TSONGAZACHE MUCHI ISLAM TAHIRA PARWEZ Asilam amakhulupilira ndi kutsatira Muhammad (S.A.W) kuti ndi mtumiki omaliza, ndiposo quran ndi Buku lomaliza, kuchokera kwa Allah. Yense omwe atasintha liu kapena mau amumabuku opatulika ai akankhidwa patali ndi chipembezo cha chi Islam. Chi Islam, monga zipembezo zinazache, zilindi tsongazache zomwe zimasunga ulemelero wache kuza chinyengo monga aneneri onyenga uchokera chiyambi chazipembezo. Zambiri mwaizi zipembezo zo nyenga mwaturuka zinthu zo nyasa anthu ndi ku zikana koma ambiri ndiochenjera kenaka zeru za ndale kumaesa kuti aike muchipembezo. Mau ochokera kwa Allama Iqbal Mundizo tizaona umu. Chi*****wa chopezeka gulula (MULLAHISM) kuonoengeka kwa chipembezo pamodzi ndi azibusa ndi Aslam chi*****wa chamsokonezo, ndi aneneri onyenga. Musaylima, Sadjah, Al-Aswad al-Ansi ndi Tulayha bin khuwaylid onsewa nthawi yao anadzicha aneneri pambuyo atamwalila Muhammad (S.A.W) awa onse amaitanidewa kuti ndi (Ridda) omwe sakuvomera lamulo kuchokela ku Medina chi*****wa chokanira mitundi ndi kusankhana kwamadera. Al-Aswad (wa chinyengo) anali msogoleri oyamba wa (ridda) dziko la Yemen. Wa chinyengo yu sakudziwika ngati adali mu Islam. Chi*****wa anali lyeyu wa maloto monga ng’anga yamaula (Kahin). Iyeyo anali kunyengeza anthu mdzina la Mulungu (Allah) anali kuombeza ndi dzanja lache. Pambuyo pa kupha umodzi wa kwao (Sahar) ataona akhale iye mmalo mwa Muhammad (S.A.W), anakhala pautsogoleri uyu Al-aswad mneneri onyenga miyezi yochepa kenaka mkadzi omwe anakwatila dzinalache ndi (SAHAR) anaganiza zakupha mwamuna wake, pombo Al-Aswad anaphedwa. Musaylima (Al-Kazab) anazicha mneneri onyenga nayenso pambuyo pa kufa kwa (Howda) anafunisitsa kuti naeso akhale msogoleli wa (Banu Hanifa) chaka 630 AD iye yu amapanga zamapemphero kataatu basi patsiku, kumanga kusiyakudya ndikusiya pangono kumwa vinyu (Wine). Analiso okhulupilira kuti munthu akamwalira azauka kwakufa. Analemba kalata kwa mtumiki wathu Muhammad (S.A.W) chaka cha 632 AD kufunitsitisa kuti naenso amulole kukhala mneneri, koma mtumiki Muhammad (S.A.W) ana kana ndi kumzuzula. Nthawi yomweyo Abubakari (RTU) anatuma Khalid Bin Walid (RTU) pamodzi ndi asikari ambirimbiri kuti akagwebane nae. Kenaka asana mwalire mkadzi wake anali ndi (SAJDAH) pomweo Musyalima anaphedwa. Naeso mkadzi wake ana zicha mneneri pambuyo pakufa mwamunawake, kulalikira mtundu wao wa (TAMIM) Al-Harith bin Said naenso ana dzicha mneneri nthani yankhondo mtundu wa Ummayah (Caliph), ABD Al-Malik bin Marwan. Asilikari ambiri naonso anali ogwirizana nae kuti ndi mneneri. Koma anamkwanisa kumgonjetsa mpakana anamupha chaka cha 698-699 A.D. Immam abu Hanifa ndiwa chikhulupiliro kuti Muhammad (S.A.W) ndi mtumiki
womalidza (Khutum-E-Nubuwat) anapeleka (Fatwa) kuti muslam aliye nse omwe azachoka mmalamulo achipembezo ndikudzicha iye yo mneneri, ai kulibwino abweretse umboni ndithu okwana. Anthu ambiri ozicha aneneri onyenga ana chulukira munthawi ya 699-767 A.D. Tione nalonso gurula Shia uyu Al-Mukhtar bin Abi Ubayd nae anazicha mneneri koma osewa ndi onyenga. Muhammad bin said (Al-Muslub) naye anali mmodzi omwe anali osokoneza osintha ma Hadith. Anaononga Hadith ndi kusintha sintha monga hadith iyi ndiena mahadith;- “Ine ndine mtumiki omalidza kuribe wina azabwera ineyo ndita mwalira” iyeyu anaongezera mauake kut:- “pokhapo Allah ankafuna kuika wina” naeso uyu anali kuzi cha mneneri moonjezera mahadith chi*****wa chofuna kuononga chipembezo cha Islam. Abu Jafar Al- Mansur (Caliph) wa Abbasid adalamulira asilikari kuti aphedwe, atafa uyu naeso Hashim bin Al-Mahadi. Hashim anali ndi anthu omutsatira mumzindamo, kenaka anagwidwa ndi kunyongedwa mchaka cha 779-780 A.D Mahmud bin Al-Faraj nae anatulukira mumdzinda wa Samara mchaka cha 849-850 A.D omwe anati Quran inafikila mwaiye kuchokera kwa Allah upitila kwa Gabriel. Nae adali ndiomtsatira ambiri mumdzinda wa Samara ndi Bagdad. Kenaka sipanapite nthawi anaphedwa ndi kunyongedwa, Caliph Al-Mutawakkil analamulira kuti aphedwe. Mirza Ali Muhammad oitanidwa (bab) chitseko, iyeyu ana badwa chaka cha 1819 A.D anali umoyo wake ku Shiraz, Iran. Anaphudzira pakana atafika zaka 15 anayamba nchito yama londa pamodzi ndi amalume ake. Atafika zaka 22 ana kwatira ndi kubala mwana wa mwamuna omwe anafa akali wachichepekele. MaShia palipose, amakhulupilira kuti kuli ma Immam obisika monga mchaka 1260 Hijra (1844 A.D) 121 zinali panthawi ya chisangalaro pomwe anasowa. Nthawi yomwe monga ya chisangalaro mwachizolowezi chaka ndi chaka, Bab anazicha kuti iyeyo ndi Imam wa 12 onse akulu akulu ma (Sheikh) ansembe anamulandira chi*****wa chaboza lache. Ambiri anayamba kudabwa naye chi*****wa Imam wa 12 azakhala osiyana ma bweledwe monga (Hurqalya) sazabwera monga munthu monga iyeyu. Chi*****wa chochenjera kulankhula izindi izi ugonjetsa ose akulu ansembe, anati ndine (Nuqtiyiula) mmodzi mwadzina la mtumiki Muhammad (S.A.W) naeso ati Quran ndi (Sharia) malamulo tsopano asintha. Koma otsatira guru la Shia ndi Sunni makamaka ansembe anamuyesa wamisala openga pomwepo adaponyedwa mdende nthawi ndi nthawi kenaka analamulidwa kuti aombeledwe futi afe, chaka cha 1850. Mirza Husayn Ali (Bahaullah) anabadwa mchaka cha 1817 mumdzinda wa Tehran. Iyeyu anali mwana oyamba kubadwa wa Mirza Abbas waku Nur, Aduna yanyumba ya malamuro. Anaphudzira akali mwana panyumba basi. Iyeyu anali pambuyo pa bab naeso analowa mdende chaka cha 1852 chi*****wa chofuna kupha Shah. Bahaullah akali mdende adali ofooka chi*****wa chamatenda kenaka adamthawitsira kudziko la Bagdad kuti asanyongedwe. Adapulumutsidwa ndi anthu aku Rusia A Minister. Nthawi atafika ku Bagdad, Asilam sanakondwe ndi uphunzitsi wake kenaka Mfumu yandodo inaganiza kuti achoke mwao mu Bagdad adamuthamangitsa kuti apite ku Constantinople ndi ku Adionople. Chaka cha 1863, pambuyo pomuthamangisa mu Bagdad, akali mjira anati lerolino ndine mneneri ndi poso mtumiki wa Mulungu (kalingana momwe ananenera Bab) koma osewa anavomera inde ndimwe mneneri, kotero ndife ma Bahais. Patapita nthawi msokonezo unayamba pakati paiwo chi*****wa odzodza uneneri kuchokera kwa Bab ayenera kukhala ndi Mirza Yah- ya osati Bahaullah ai.
Ose anthu anasintha ndi kutsatira Mirza Yahya kumusiya uyu onyenga Bahaullah komwe ku Turk. Boma la Turk linapepha kuti onse otsatira Babi ndi Bahai achoke muno mwathu mu Adrianaple. Koma Bahaullah adathawira ku Akka (Acre) mudziko la Palestine pafupi ndi ndende. Chaka cha 1868 Mirza Yahya ndiotsatira ache adapita ku Cyprus. Koma chodabwitsa mchaka cha 1892 Bahaullah adamwalira koma Abdul Baha (Abbas Effendi) adatenga malo udziyetsa naeso mneneri. Chaka cha 1921 Abdul Bahadaamwalira, maloache akulowa mzukulu dzina lache ndi Shoghi Effendi naeso amwalira chaka 1957 akalibe kubeleka kapena olowa chokoro. Koma mpakana lero lino utsogoleri uyendetsedwa ndi guuru (Universal House of Justice). Mirza Ghulam Ahmad anabadwa mumdzinda wa Qadiyan mudziko la India, chaka cha 1830. Adapata maphudziro ndi ma Shie ndi ma Sunni. Atatha adalowa nchito ya ukalembera ya Comishona waku Sialkoto koma anagwa mayeso katatu kuti apezenchito yapamwamba. Kenaka, ankafunitsitsa kuyamba zaulaliki upyolera mu studio. Iyeyo anali kupezeka ndi mbusa Rev. Butler omwe anali mu Kristo wa Mission. Koma adapeza mpata wina kwa Komisione wa chibili. Koma mchaka cha 1876 Ghulam Ahmad ahmad adleka nchito ndi kubwelera ku Qadiyani pambuyo atamwalira bambo wake. Patapita zaka zambiri , anazicha munthu ophudzira, mbusa, mphudzitsi (Bait) ochinjiliza chipembezo kenaka kusintha malamuro monga momwe ankachitira Bab ndikuzicha mneneri Mahdi, kenaka mneneri. Ena mwabanja lache monga mkadzi oyamba ndi adia ana anakana kuti avomere za uneneri wake. Koma ena onse adamtsarira iyeyu ndikuzicha iwowo ndi Aslam koma ena sanavomere zakuti iyeyu ndi mneneri ai adawacha ma (Kafir). Asilamu enIenI anati Ghulam Ahmad ndi ose omutsatira ndi ma Kafir si Asilamu ai, mpakana lero Asilamu onse akukana kuti iwowo Sali Aslam ai aguulula Ghulam Ahmad. Ghulam Ahmad andamwalira chaka cha 1908 kumatenda ya chipindupindu (cholera) ndi kutsegura mmimba, ndipo adafa olumala, Diabetes, ndiopenga (Dementia). Patapita dzaka zambiri. Ata mwalira Ghulam Ahmad otsatira ache adagawanika maguuru awiri monga 1 = Qadian 2 = Lahoris. Chimodzi modzi monga (Zorasterism, Judaism, Christianity, Chaldean, ndi Sabean zipembezo) naoso adapita mmabvuto monga omwewa talankhula, magulu ndi midzi ataikana ndie zosezi tanazi njira yokha yokha yobasi ndi chipembezo cha Islam, chomwe chilindi mneneri aona, omali za Muhammad (S.A.W) Mulungu ekha ndiye omwe adzetsa mabvuto ya (Earthquake) ndi zina zache. Koma aneneri onyenga anayamba kale chiyambi cha Judaism. Allama Iqbal ati: zosezi ndizo nyatsa kwabasi muchi Islam. Msokonezo mkati mwa a Shia aku iran ndi maphudzitso awo amaononga chipembezo (Buruz Hulul, Zill). Chimodzi modziso monga guru la sunni ugawanikana ma guru ambiri ndi ma Sufi monga otsatira za Chilla, Kashaf, Ilham, kukhala pamodzi ndi chipembezo cha Islam. Koma Bahai ndi Ahmadi akalipo chi*****wa cha umbuli wa Mullahism ndi thandizo uchokela ku Britain. Omwe Ali Asilam, onse padziko lapasi akukana kuti awa ma Qadiani ndi ma Bahai kuma Britain akali kuwathandiza iwowo. Angakhale zitero anthuwa amango chepekela pang’ono pang’ono mphabvu za ulaliki zikuchepekera kwa iwowo.
MABUUKU ENA . Roohani Khazain by Mirza Ghulam A. Qadiani . BAhaullah and the new era By J.E. Esselemont . Qadianies and the Orthodox Muslims by Iqbal . Jhootey nabi false prophets by Rafiq Dilawari . Talbess-E-Iblees by Rafiq Dilawari Translated in Nyanja by : OLEMBA NDINE SHEIKH ASSADULLAH MWALE MUFTI OF ZAMBIA P. O. BOX FW 306 LUSAKA – ZAMBIA CELL: +260 97 7493870 EMAIL:assadullahmwale@yahoo.com Anti Ahmadiyya Movement in Islam Dr Syed Rashid Ali P.O.Box 11560 Dibba Al Fujairah United Arab Emirates. E-mail: rasyed@emirates.net.ae / alhafeez.org/rashid » تاريخ النشر: 25-11-2009 » تاريخ الحفظ: » شبكة ضد الإلحاد Anti Atheism |