TAHIRA PARWEZ
Asilam amakhulupilira ndi kutsatira Muhammad (S.A.W) kuti ndi mtumiki omaliza,
ndiposo quran ndi Buku lomaliza, kuchokera kwa Allah. Yense omwe atasintha liu
kapena mau amumabuku opatulika ai akankhidwa patali ndi chipembezo cha chi Islam.
Chi Islam, monga zipembezo zinazache, zilindi tsongazache zomwe zimasunga
ulemelero wache kuza chinyengo monga aneneri onyenga uchokera chiyambi
chazipembezo. Zambiri mwaizi zipembezo zo nyenga mwaturuka zinthu zo nyasa anthu
ndi ku zikana koma ambiri ndiochenjera kenaka zeru za ndale kumaesa kuti aike
muchipembezo. Mau ochokera kwa Allama Iqbal Mundizo tizaona umu. Chi*****wa
chopezeka gulula (MULLAHISM) kuonoengeka kwa chipembezo pamodzi ndi azibusa
ndi Aslam chi*****wa chamsokonezo, ndi aneneri onyenga.
Musaylima, Sadjah, Al-Aswad al-Ansi ndi Tulayha bin khuwaylid onsewa nthawi yao
anadzicha aneneri pambuyo atamwalila Muhammad (S.A.W) awa onse amaitanidewa
kuti ndi (Ridda) omwe sakuvomera lamulo kuchokela ku Medina chi*****wa chokanira
mitundi ndi kusankhana kwamadera. Al-Aswad (wa chinyengo) anali msogoleri oyamba
wa (ridda) dziko la Yemen. Wa chinyengo yu sakudziwika ngati adali mu Islam.
Chi*****wa anali lyeyu wa maloto monga ng’anga yamaula (Kahin). Iyeyo anali
kunyengeza anthu mdzina la Mulungu (Allah) anali kuombeza ndi dzanja lache.
Pambuyo pa kupha umodzi wa kwao (Sahar) ataona akhale iye mmalo mwa Muhammad
(S.A.W), anakhala pautsogoleri uyu Al-aswad mneneri onyenga miyezi yochepa kenaka
mkadzi omwe anakwatila dzinalache ndi (SAHAR) anaganiza zakupha mwamuna wake,
pombo Al-Aswad anaphedwa.
Musaylima (Al-Kazab) anazicha mneneri onyenga nayenso pambuyo pa kufa kwa
(Howda) anafunisitsa kuti naeso akhale msogoleli wa (Banu Hanifa) chaka 630 AD iye
yu amapanga zamapemphero kataatu basi patsiku, kumanga kusiyakudya ndikusiya
pangono kumwa vinyu (Wine). Analiso okhulupilira kuti munthu akamwalira azauka
kwakufa. Analemba kalata kwa mtumiki wathu Muhammad (S.A.W) chaka cha 632 AD
kufunitsitisa kuti naenso amulole kukhala mneneri, koma mtumiki Muhammad (S.A.W)
ana kana ndi kumzuzula. Nthawi yomweyo Abubakari (RTU) anatuma Khalid Bin Walid
(RTU) pamodzi ndi asikari ambirimbiri kuti akagwebane nae. Kenaka asana mwalire
mkadzi wake anali ndi (SAJDAH) pomweo Musyalima anaphedwa. Naeso mkadzi wake
ana zicha mneneri pambuyo pakufa mwamunawake, kulalikira mtundu wao wa
(TAMIM)
Al-Harith bin Said naenso ana dzicha mneneri nthani yankhondo mtundu wa Ummayah
(Caliph), ABD Al-Malik bin Marwan. Asilikari ambiri naonso anali ogwirizana nae kuti
ndi mneneri. Koma anamkwanisa kumgonjetsa mpakana anamupha chaka cha 698-699
A.D. Immam abu Hanifa ndiwa chikhulupiliro kuti Muhammad (S.A.W) ndi mtumiki
womalidza (Khutum-E-Nubuwat) anapeleka (Fatwa) kuti muslam aliye nse omwe
azachoka mmalamulo achipembezo ndikudzicha iye yo mneneri, ai kulibwino abweretse
umboni ndithu okwana. Anthu ambiri ozicha aneneri onyenga ana chulukira munthawi ya
699-767 A.D. Tione nalonso gurula Shia uyu Al-Mukhtar bin Abi Ubayd nae anazicha
mneneri koma osewa ndi onyenga.
Muhammad bin said (Al-Muslub) naye anali mmodzi omwe anali osokoneza osintha ma
Hadith. Anaononga Hadith ndi kusintha sintha monga hadith iyi ndiena mahadith;- “Ine
ndine mtumiki omalidza kuribe wina azabwera ineyo ndita mwalira” iyeyu anaongezera
mauake kut:- “pokhapo Allah ankafuna kuika wina” naeso uyu anali kuzi cha mneneri
moonjezera mahadith chi*****wa chofuna kuononga chipembezo cha Islam. Abu Jafar Al-
Mansur (Caliph) wa Abbasid adalamulira asilikari kuti aphedwe, atafa uyu naeso Hashim
bin Al-Mahadi. Hashim anali ndi anthu omutsatira mumzindamo, kenaka anagwidwa ndi
kunyongedwa mchaka cha 779-780 A.D
Mahmud bin Al-Faraj nae anatulukira mumdzinda wa Samara mchaka cha 849-850 A.D
omwe anati Quran inafikila mwaiye kuchokera kwa Allah upitila kwa Gabriel. Nae adali
ndiomtsatira ambiri mumdzinda wa Samara ndi Bagdad. Kenaka sipanapite nthawi
anaphedwa ndi kunyongedwa, Caliph Al-Mutawakkil analamulira kuti aphedwe.
Mirza Ali Muhammad oitanidwa (bab) chitseko, iyeyu ana badwa chaka cha 1819 A.D
anali umoyo wake ku Shiraz, Iran. Anaphudzira pakana atafika zaka 15 anayamba nchito
yama londa pamodzi ndi amalume ake. Atafika zaka 22 ana kwatira ndi kubala mwana
wa mwamuna omwe anafa akali wachichepekele. MaShia palipose, amakhulupilira kuti
kuli ma Immam obisika monga mchaka 1260 Hijra (1844 A.D) 121 zinali panthawi ya
chisangalaro pomwe anasowa. Nthawi yomwe monga ya chisangalaro mwachizolowezi
chaka ndi chaka, Bab anazicha kuti iyeyo ndi Imam wa 12 onse akulu akulu ma (Sheikh)
ansembe anamulandira chi*****wa chaboza lache. Ambiri anayamba kudabwa naye
chi*****wa Imam wa 12 azakhala osiyana ma bweledwe monga (Hurqalya) sazabwera
monga munthu monga iyeyu.
Chi*****wa chochenjera kulankhula izindi izi ugonjetsa ose akulu ansembe, anati ndine
(Nuqtiyiula) mmodzi mwadzina la mtumiki Muhammad (S.A.W) naeso ati Quran ndi
(Sharia) malamulo tsopano asintha. Koma otsatira guru la Shia ndi Sunni makamaka
ansembe anamuyesa wamisala openga pomwepo adaponyedwa mdende nthawi ndi
nthawi kenaka analamulidwa kuti aombeledwe futi afe, chaka cha 1850.
Mirza Husayn Ali (Bahaullah) anabadwa mchaka cha 1817 mumdzinda wa Tehran.
Iyeyu anali mwana oyamba kubadwa wa Mirza Abbas waku Nur, Aduna yanyumba ya
malamuro. Anaphudzira akali mwana panyumba basi. Iyeyu anali pambuyo pa bab
naeso analowa mdende chaka cha 1852 chi*****wa chofuna kupha Shah. Bahaullah akali
mdende adali ofooka chi*****wa chamatenda kenaka adamthawitsira kudziko la Bagdad
kuti asanyongedwe. Adapulumutsidwa ndi anthu aku Rusia A Minister. Nthawi atafika
ku Bagdad, Asilam sanakondwe ndi uphunzitsi wake kenaka Mfumu yandodo inaganiza
kuti achoke mwao mu Bagdad adamuthamangitsa kuti apite ku Constantinople ndi ku
Adionople. Chaka cha 1863, pambuyo pomuthamangisa mu Bagdad, akali mjira anati
lerolino ndine mneneri ndi poso mtumiki wa Mulungu (kalingana momwe ananenera
Bab) koma osewa anavomera inde ndimwe mneneri, kotero ndife ma Bahais. Patapita
nthawi msokonezo unayamba pakati paiwo chi*****wa odzodza uneneri kuchokera kwa
Bab ayenera kukhala ndi Mirza Yah- ya osati Bahaullah ai.
Ose anthu anasintha ndi kutsatira Mirza Yahya kumusiya uyu onyenga Bahaullah komwe
ku Turk. Boma la Turk linapepha kuti onse otsatira Babi ndi Bahai achoke muno
mwathu mu Adrianaple. Koma Bahaullah adathawira ku Akka (Acre) mudziko la
Palestine pafupi ndi ndende.
Chaka cha 1868 Mirza Yahya ndiotsatira ache adapita ku Cyprus. Koma chodabwitsa
mchaka cha 1892 Bahaullah adamwalira koma Abdul Baha (Abbas Effendi) adatenga
malo udziyetsa naeso mneneri. Chaka cha 1921 Abdul Bahadaamwalira, maloache
akulowa mzukulu dzina lache ndi Shoghi Effendi naeso amwalira chaka 1957 akalibe
kubeleka kapena olowa chokoro. Koma mpakana lero lino utsogoleri uyendetsedwa ndi
guuru (Universal House of Justice).
Mirza Ghulam Ahmad anabadwa mumdzinda wa Qadiyan mudziko la India, chaka cha
1830. Adapata maphudziro ndi ma Shie ndi ma Sunni. Atatha adalowa nchito ya
ukalembera ya Comishona waku Sialkoto koma anagwa mayeso katatu kuti apezenchito
yapamwamba. Kenaka, ankafunitsitsa kuyamba zaulaliki upyolera mu studio. Iyeyo
anali kupezeka ndi mbusa Rev. Butler omwe anali mu Kristo wa Mission. Koma adapeza
mpata wina kwa Komisione wa chibili. Koma mchaka cha 1876 Ghulam Ahmad ahmad
adleka nchito ndi kubwelera ku Qadiyani pambuyo atamwalira bambo wake.
Patapita zaka zambiri , anazicha munthu ophudzira, mbusa, mphudzitsi (Bait) ochinjiliza
chipembezo kenaka kusintha malamuro monga momwe ankachitira Bab ndikuzicha
mneneri Mahdi, kenaka mneneri. Ena mwabanja lache monga mkadzi oyamba ndi adia
ana anakana kuti avomere za uneneri wake. Koma ena onse adamtsarira iyeyu ndikuzicha
iwowo ndi Aslam koma ena sanavomere zakuti iyeyu ndi mneneri ai adawacha ma
(Kafir).
Asilamu enIenI anati Ghulam Ahmad ndi ose omutsatira ndi ma Kafir si Asilamu ai,
mpakana lero Asilamu onse akukana kuti iwowo Sali Aslam ai aguulula Ghulam Ahmad.
Ghulam Ahmad andamwalira chaka cha 1908 kumatenda ya chipindupindu (cholera) ndi
kutsegura mmimba, ndipo adafa olumala, Diabetes, ndiopenga (Dementia). Patapita
dzaka zambiri. Ata mwalira Ghulam Ahmad otsatira ache adagawanika maguuru awiri
monga 1 = Qadian 2 = Lahoris.
Chimodzi modzi monga (Zorasterism, Judaism, Christianity, Chaldean, ndi Sabean
zipembezo) naoso adapita mmabvuto monga omwewa talankhula, magulu ndi midzi
ataikana ndie zosezi tanazi njira yokha yokha yobasi ndi chipembezo cha Islam, chomwe
chilindi mneneri aona, omali za Muhammad (S.A.W) Mulungu ekha ndiye omwe adzetsa
mabvuto ya (Earthquake) ndi zina zache. Koma aneneri onyenga anayamba kale
chiyambi cha Judaism.
Allama Iqbal ati: zosezi ndizo nyatsa kwabasi muchi Islam. Msokonezo mkati mwa a
Shia aku iran ndi maphudzitso awo amaononga chipembezo (Buruz Hulul, Zill).
Chimodzi modziso monga guru la sunni ugawanikana ma guru ambiri ndi ma Sufi monga
otsatira za Chilla, Kashaf, Ilham, kukhala pamodzi ndi chipembezo cha Islam. Koma
Bahai ndi Ahmadi akalipo chi*****wa cha umbuli wa Mullahism ndi thandizo uchokela ku
Britain.
Omwe Ali Asilam, onse padziko lapasi akukana kuti awa ma Qadiani ndi ma Bahai kuma
Britain akali kuwathandiza iwowo. Angakhale zitero anthuwa amango chepekela
pang’ono pang’ono mphabvu za ulaliki zikuchepekera kwa iwowo.
MABUUKU ENA