عرض المقال :Where is the Grave of Jesus
  الصفحة الرئيسية » مـقـالات الموقـــع » كشف البلية بفضح الأحمدية » Non - Arabic Articles » Nayanga/Chichewa

اسم المقال : Where is the Grave of Jesus
كاتب المقال: webmaster

Bismillah Al-Rahaman Al-Raheem

Anti Ahmadiyya Movement in Islam

Kodi manda ya Yesu Yalikuti ?

(Funso kwa Ahmadiyya)

(Olemba ndi Dr. Rashid

(Translated from English in Nyanja by H.E Mufti Assadullah Mwale)

Mbale Qadiani ndi Ahmadiyya,

Madalitso afikire kwa otsatira chilungamo

Mirza Ghulam Ahmad Qadiani,omwe anayambisa guulu la Ahmadiyya Movement akuzitama motere :

« Mulungu ana ndivumbilitsila kuti mesaya Yesu mwana wa Maria anafa ». (Tauzeeh-e-Maram, Roohani Khazain Volume 3 p 402).

Mirza Ghulam Anati :-

« Ndaudzidwa komwe kuli manda ya Yesu (ku Kashmir), ndipo Qur’an yanena uchokera kwa Mulungu kuti Yesu anafa » (Roohani Khazain Volume 18 p 358-361).

Kodi ndi manda ya Yesu iyi ?

« Manda a Yesu » (7/24) pakati pa chikristu ndi mbili yakalekale pafupifupi kwa nkhani yache kumapeto. Anzeru ochokau Oxford University akali yakaliyakali ufunitsitsamolo amandaeni eni pafupi ndi mzindawa Yerusalem, pakachisi ina yake, akuti apondiye pomwe palimanda Yesu.

Kekale munthuwina ochedwa Martin Biddle pamodzi ndimkadzi wake Birthe Kjolbye Biddle, anapeza zidutswa zamala otsekera uja ndi zinazake mpakanamuno mu 19th Century kapena « Kanyumba kangoono » kofanan ndi manda a Yesu. Mpakana lelolino ambiri akuisimikiza kuti ndipomwe Yesu anaikidwa.

http:/w.w.w.pbs.org/WHATSON/press/jul01/secretsofdead.html

Muti bwanji kwaizi ?

Mwina manda a Yesu ali ku Kashmir ?

Ina website yochedwa « Tomb of JESUS « Manda a Yesu, yomwe ingatitsimikidzire ngati manda a Yesu ali ku Kashmir

Koma mwinewaiyi website ankabisara kenaka adaonekera poyera kutinayenso ndimmodzi wa guulu la Ahmadiyya ndipowapafupi ndi Mirza Ghulam monga khalifa wake, iyeyu akuti :-Bodzalake:-

« Nthawi yomwe Yesu ankapulumuka pamtandapaja, anthawira kudzikola Kashmir, komwe adakhalaumoyo wake ose. Komweko ku Kashmir, anali kulalikira mau a Mulungu ku mtundu wa Ayuda. Akutero, Yesu anakwatira komwekoku Kashmir mkadzi dzinalache Maryani anapeza dzipatso za ana ndikubala ana ambiri mbiri komweko ku Kashmir, anafa Yesu alindi dzaka izo, manda a Yesu alipamalo ochedwa Mohala Kan Yar District mzindawaukulu Srinagar, jammu ndi Kashmir, Northern India, pomwepolero apaitana kuti Roza Bal (« Mandaoyera »).

Http//w.w.w.tombofjesus.com/welcomeall.htm

« Malo awa awoneka kuti siamuthu kapena achipembezo chinachache kapena guulu lililonse kapena pomwe Yesu anaikidwa kapena wina wache aliyense ».

Ndizoveka kuti uyu Mirza ndi mmodzi wa guulu la Qadiani.

Mirza akuti :- « Omwe sanabadwe mguulu la Ahmadiyya, sazakaona ubwino wa Imaam Mahdi »

Nanga iwe muthu wa kuda (Black) omwe ulimguulu la Ahmadiyya ulipati ? Ukudziwa kuti awa mapunjabi Pakistan ndi achinyengo ?

(Source : posting of 9/9/2000 in Lahore, Ahmadiyya Message Board)

Onseotsitira guulu Lahori ndi Qadiani akhulupira kuti Yesu bin Maryam (AS) anafela ku Kashmir. Kodi awa anthu akhulupilira ziti ? Ndi chi*****wa chakutimsogoleri wao Mirza Ghulam Ahmad Qadiani anatero, ndiye chi*****wa chaichi onse alinjira imodzi yotaika. Kodi sindi kutero ?

Mwine wamanda akuti :-

« Zatsimikizidwa kuti palibe chikaiko chomwe adanena Hazrat Ahmad ndi zoona ndiponso mmbiri yakale kuti Yesu anailidwa mmanda ku Kashmir. Aliyense omwe angathe kulembankhani za Yesu ku India azalemba zaku Kashmir zomwe anauzidwa ndi Mirza Ghulam Ahmad Qadiani. Chimodzi modzi naeso Mulla Nadri dniera.

(Source : posting of 9/9/2000 in Lahore, Ahmadiyya Message Board)

Kodipalibe mmodzi Qadian omweanayesa kapena uyesa upenyetsetse zomwe analemba ulingana ndi manda ya Yesu, kodi ndi zoona ? Sanaone, ai ndiotembeleledwa chao palibe.

Kalembedwe ka Mirza Ghulam ndikodabwitsa chi*****wa amazitutsa iyemwini, tikaona akulu awa anati mumalemba awo, kuti Yesu alindi malo amanda patatu kapena atatu

Kodi ndi malo ati enieni a manda ya Yesu ?

(a) Manda a Yesu ku Al-Khaleeli (Gulailee) :

Mirza Ghulam ati :-

Chaka cha 1891 Mirza Ghulam analembabuuku la Izala Auham lomwe lilindima page 948. Momwemu anati Yesu sanatengedwe wa moyo upita ku mwamba mongamomwe aslamu amakhulupilira. Koma iye Mrza akuti anamwalira pamtanda ndikuikidwa mu manda kwao.

Anati Mirza Ghulam :-

« Yesu anapita kwao ndi kufa komweko, akutero. Komasosi uchoona kuti thupi limodzi lomwe linaikidwa mmanda, linaukaso ai …..acts 1 :3 ndiye umboni kuti thupi la Yesu linaikidwa ku Al-Khaleeli (Gulailee). Ata mwalira Yesu anaonekera kwa ophunzira ake monga (kashf) mchiganiziro kwa matsiku 40 » (Izala-e-Auham, Roohani Khazain volume 3 pages 353 – 354).

(b) Manda a Yesu ku Quds :

Mirza Ghulam akuti :-

« Patapita dzaka zitatu mu 1894, Mirza anasintha kalembedwe mbuuku la Atmam-e-Hujjat (Roohani Khazain Volume 8) ati Yesu anafa.

« Anati ndi kutsimikizirani izi kuti Yesu anaikidwa ku Quds. Manda a Yesu a Yesu zoonaaliku Quds. Chi*****wa Yesu anabadwira ku Beterehem ndiye Beterehem ndi Quds palimtunda okwana 30 miles ndieno manda a Yesu alikomweko, pamandapo pali kachisi anamanga yaikulu upambana makchisi yonse. Mkati mwake muli manda a Yesu ndi manda a Maria. Koma choonadi manda awiri sali pamodzi ai ».

(c) Manda a Yesu ku Kashmir :

Mirza Ghulam akuti :-

« Patapita dzaka 8 mu 1899, Mirza Ghulam anasintha kalembedwe anati Yesu manda yake yali ku Kashmir ndiye kwomwe anaikidwa kuja ku india.

Ndi kunena choonapatapita dzaka 8, kuti Yesu adathawira ku Kashmir pambuyo pokha.

Wassalam

Anti Ahmadiyya Movement in Islam.

Dr.Syed Rashid Ali

P.O.Box 11560

Dibba Al Fujairah

United Arab Emirates (UAE)

rasyed@emirates.net.ae

http://alhafeez.org/rashid/

اضيف بواسطة :   admin       رتبته (   الادارة )
التقييم: 0 /5 ( 0 صوت )

تاريخ الاضافة: 26-11-2009

الزوار: 2563


جديد قسم مـقـالات الموقـــع
القائمة الرئيسية
البحث
البحث في
القائمة البريدية

اشتراك

الغاء الاشتراك