Anti Ahmadiyya Mouvement in Islam
KAMBA MOLEMBA
KUBADWA KWA MIRZA GHULAM
CHIYAMBI CHA UMOYO WA MIRZA QADIANI
« Ndina badwa mchaka cha 1839 kapena 1840 A.D ndinali umodzi wa ana amapasa.
Wina mwaine anali mkadzi dzinalache ndi Jannat (paradiso). Mkati mwa malemba akuti
« Ya adam uskun antaa wa zaujoka al-jannah, » zomwe zinavumbulutsidwa mu Braheen Ahmadiyya tsamba la 496 zaka 20 zapita, mau akuti « Jannat » adatenga malo
aku ulu kotelo kuti mapasa wamkadzi adapasidwa zinalo, ndipo uyu mapasa anafa ali ndi
miyezi 7 ». (Tiryaq-ul-quloob, roohani kazain vol. 15 Tsamba la 479 olemba Mirza Ghulam Ahmad Qadiani).
« Bambo wanga ndi Mirza Ghulam khazain, anali ndi chuma ndipo otchuuka. Onyamata
wanga ndi naphudzila ndili ndizaka 6 – 7 ndi mphunzisi waku Persian omwe adapatsidwa
kuti andi phyzise qurran monga wa nchito ndi ma book ya lilime la persian. Dzina la
mphutsi ndi fazl llahi. Nditafika dzaka 10 khumi, ana pezeka wina mphuzitsi wachiarab
omwe ndi moulvi, kuti naeso andi phuzise, dzinalache ndi Fazl Ahmad. Pomwe ndinali
ndi zaka 17 – 18, ndina pitiliza maphuzilo kuchokela kwa a bambo anga. Ndi napata
maphuzilo a grammer, logic ndi hikmat (medicine) ndi ena ma buuku a medicine ku
phuzisidwa ndi a abambo anga. Chi*****wa cho fooka kwa nthanzi, abambo anga
ankandiletsa kuwelenga ko pitilira malile.
« Nthawi yomwe azuungu achi Britishi adalanda mudzi wathu, abambo anga ada
mangala ku khoti ya azuungu kuti ababwezele. Ni dakhala ndi mpata oima kuimilira
mulandu omweuyu. Ngakhale zinali zo nditangwanisa umoyo wanga ndiponso sindi
nafune kuti ndipitilize umoyo wanga pamalo monga awa apamudzi, koma ndi
dakakamizidwa kuionela mudzi ndi zina zofunikila momwemo. Pomwepo ndinali
kugwila nchito ndi azuungu achi british government zaka zo chepa ku Sialkot khoti
monga kalembela malipilo ya Rs. 15/- pa mwezi.
« Sipanapite masiku ambiri ndi nasiya nchito ndi nabwerela ku Nkhani zaku mudzi.
Nthawi ndinali kuganiza thandauzo la buuku la Quran (tafseer). Pomwe ndinafika zaka
30 – 35 abambo anga adamwarila, zidandifikira zimwetumwetu zolankhula ndi
Mulungu (Mukalimat-e-llahiah) kopanda marile ».
(Kitab-ul-bariayh pp. 134 – 136 ndemanga Mirza Ghulam Ahmad Qadiani, Roohani
Khazain vol. 13 page 180, Tuzuk-E-Ahmadi yolembedwa ndi Akhbar-al-hakam Qadiani
yochu uka nambala vol. 37 nambala 18519 tsikula 21 – 28 May 1934 A.D).
MIRZA AKOKEDWA NDI NDALAMA ZA PENSHIONI.
« Bismillah ar-rahman ar-raheem. Hazarat waalida sahiba (olemekezeka amai akazi a
Mirza Ghulam) anati kwaine, nthawi ina ndikali mnyamata, pomwe Hazat Masseh
Mowood anapita ukatenga ndalama za ambuye ako za penshioni, a Mirza Imamdeen
(muphwa wa Mirza Ghulam) ada londola iye ukatenga makhobili.
Koma nthani yomwe yotenga ndalama za penshioni anaona kuti zina zachesizili bwino ai
koma anamatenga (Mirza) mmalo mwa Qadiani, adazweta nayeapa ndi apa mpaka
momwe ndalama zija zitatha, ndipo imamdeen anaona kuti zinthu sizili bwino pomwepo
ana thawira malo ena ndikumsiya ekha. Hazarat Maseeh Mowood zidamvuta kuti
abwelele kunyumba chi*****wa chakuti ndalama zonse zidatha anamva manyazi chi*****wa
ambuye ache anamfunitsitsa kuti abwelele pa nchito, komabe adayamba nchito kukhoti
kwa achiwili wa comishiona boma ya Sialkoti kwa malipilo yochepa”.
(Seeratul mahdi part 1 page 41 yolembedwa ndi Mirza Basher Ahmad mwana wa Mirza Basher Ahmad mwana wa Mirza Ghulam).
BANJA LA CHEEPA
Bambo wanga, Mirza Ghulam Murtuza, adakondetsetsa mpando wo khalapo kwa nduna
Darbar, anali mmodzi wachilakolako ofunila mafuno abwino a British Government ndipo
olimba mtima, koti nthawi ya chiwawa mu chaka cha 1857 A.D ankathandizila kwabasi
ufumu wa azungu ndi Boma lao, kotelokuti ada kwanisa ku gula 50 mahachi kuchosa
ndalama zake ndi kupeleka othandizila asilikali 50. Koma ufumu wa Mirza Ghulam
ndimapatoache anayamba kuchepekela tsiku ndi tsiku koti matsiku athu ndi banja ai
linayamba ku chepekela anthu adatha”. (Tohfa-e-qaiser, roohani khazain vol. 12 tsama 270-271).
“Zotuluka umo azuungu achi british adalanda zonse pamodzi ndi thaaka yomwe
pambuyo pake anati tikupatsani penshioni ya Rs, 700/-yokha pa chaka, kenaka nu
bwezaso ndalama zochepa Rs, 180/ - nthawi atamwalira ambuye anga kenaka azuunga
anati uchokela lelo taima kupeleka ndalama kulibe chanu kumalo anuwa, izi zonse
zinadza nthawi amalume anga anamwalira (akuulu a atate) atamwalira. (Seerat-ul-Mahdi part 1 page 41 olemba Mirza Basher Ahmad mwana wa Mirza Ghulam Ahmad Qadiani).
MATENDA KWA OSANKHIDWA UYO (AKUTELO).
“Mano a Mirza Ghulam Ahmad Qadiani adali owora kotelo kuti anali kupweteka
koopsya kotelokuti chi*****wa chaicho mmimba munadza matenda ama Ulcer ndiposo
lilime lache naloso linali ndi matenda ama Ulcer. (Seerat-ul-mahdi part 2 tsamba 135 olemba Mirza Basher Ahmad mwana wa Mirza Ghulam Ahmad Qadiani). Lilime linali
ku chosa mafina oopsya.
“Tsiku lina aba akuulu anagwa pa dzene ndi kuvulala koopsya kotelokuti dzanja lama
dzele ai lidathyoka, kotelo kuti dzanja lija silinagwirepo nchito inailiyense mpakana
mmanda”.
(Seeratul-mahdi part 2 tsamba 198).
KHUNYU (CHINYULUNYULU) KHUNYU
“Taonani osankhidwayo akupezeka ofoka ku ubongo, kwathawi yaitari asana peze banja. Ndidadziwakuti ndili ndimatenda a khunyu”.
(Kalata wa Mirza Ghulam Ahmad Qadiani tsiku la 22 – 02-1887 mu buuku ya Maktoobate Ahmadiyya vol. 5 tsamba 14 kuchokela buuku la Navishta-e-Ghaib olemba
Khalid Wazirabadi).
“Nthawi itafika yopeza banja mtima ndi ubongo zonse zina li zofooka ndiposo ndinali kunva chizwezwe zosezi zidandi kakamila nthawi yaitali; chi*****wa chaichi
sindinali kupumabwino ai (osa sangalala umoyo onse) chi*****wa chamanganizo
(kupenga) ndikusowa chilakolako cho kumana ndi mkadzi mpanvu za umuna
ndilibe”
(Tiryaq-ul-Quloob Roohani khazain vol. 15 tsamba 203 olemba Mirza Ghulam Ahmad Qadiani).
KALATA KWA HAKEEM NOORUDDIN, MIRZA ANATI:
“Ineyo nda chilitsidwa ndi mankhwara yako unandipatsa. Ang’ono mwamatenda monga khunyu ndi mphanvu zaumuna (Lethargy) ndi utuupa mimba (Gastric
Acidity) ai ndapola ndiku chiila. Chi*****wa chaicho nidali ndi matenda oopsya
kotelokuti madzi achimuna sanali kutuluka nthawi yokumana ndi mkadzi wanga
kenaka ndi kagona mkodzo utuluka okha. Kuchepekela mpahvu zokomana ndi
mkadzi chikufwa cha matenda omweo. Chi*****wa chaicho mankhawala ako
unandipatsa aja ai ndi kwanisa ku gwira nchito yokumana ndi mkadzi mphavu
zabwerela.
(MAKTOOBAT-E-AHMADIYYA VOL. 5 NO. 2 OSONKHANISA MA KALATA NDI
MIRZA GHULAM AHMAD QADIANI).
“Chibvumbulutso chi chabwela chi*****wa cha ukwati, nthawi iyo mtima wanga ndi ubongo ndi thupi zinali zo fooka koma kuchotsela matenda a Diabetes Mellitus ndi
matenda a chizungulire (Dizness) mmutu ndi kukhala osakondwa wamadandaulo
amtima (Depression), ndina dziwa kuti ai ndiliso ndi chifuwa chamidulo
(Tuberculosis) mwa ine.
(Nuzool-e-Maseeh, Roohani Khazain vol. 18 tsamba 587 umboni ndi Mirza Ghulam Ahmad Qadiani).
“Iyeyu Mirza Ghulam Ahmad Qadiani anali wachidule kumanga Ramadan osa kwanilisa mwezi wa Ramadan kenaka anali kulipila masiku ena popasa anthu
mwina malipiro; chi*****wa chaicho ndi matenda ake anali kugwidwa ndi khunyu
ngakhale mmwezi wa Ramadan kenaka anagwidwa ndi kumasula panthawi ya
Magrib (dzuwa litalowa). Anali akulu awa akugwidwa ndi khunyu nthawi ndi
nthawi kotelokuti umoyo wao unali mchiopsyezo kweni kweni”.
(Seerat-ul-Mahdi part 1 tsamba 51 olemba Mirza Ghulam Ahmad Qadiani).
“Hazart Sahed anali ndi matenda odetsedwa achimdulo (Chronic Melancholic). Matenda aya ndi akatengela apabanja. (Mirza Sahib sangakhale kapena kugwira
nchito ya uneneri – olemba). Mirza sahab anali ndi amalume ache (mbanja) dzina
lache anali Mirza Jamiat Baig. Anali ndi mwana wa mwamuna umodzi ndi mkadzi
umodzi ndipo osewa anali ndi matenda a misala kubongo. Mwana wa mwamuna
dzina lache ndi Mirza Sher Ali, mwana mkadzi anali Hurmat Bibi. Omwe ada
manga banja ndi Hazrat Sahab”. (Mirza ndi Hurmat Bibi – osewa anali ndimatenda ya misala!! Zamanyazi kwabasi ! nanga ana atabadwa akhala otani ? zodabwitsa kwa basi
– olemba). (Seerat-ul-Mahdi part 1 tsamba 51).
KHUNYU (MELANCH EHOLIA) MBILI YAKALE NDI MANKHWALA.
Matenda amaganizo ndi khunyu ndi amodzi matenda akale kale chiyambi cha munthu
pano padziko la pansi. Anga khale mmalemba akale zonsezi zilimo monga matenda
aubongo. Olemba akale anaikamifano chimodzi modzi zaaka zapita 2,000 ufikila 4,000
mpkana lelo.
Anga khale anthu aku Greek adalemba mdodnomeko wamatenda aya aubongo. Koma
2,300 zaaka zapita, matenda awa ozelezeka a (Psychiatric) mabvuto awa ndi ochokela
monga achifuniro o sati achilengedwe (capriciousness). 1zozo za matenda aubongo
(Psychiatric) nalero akalipobe. Makhate ndi khunyu (epilepsy), uzelezeka (Mania)
khunyu (Melancholia) ndi (Paranoia). Olemba akuti mkadzi omwe ali ndi khunyu
kapena khunyu sa mapeza turo, chakudya osakoma, angakhale lero lino zikadalipo be
(Depression).
Nthawi ya ulamuliro wa Aroma, sing’anga Galen molemba anati kumatendawa a
(Depression) ambiri odwala amaoneka a mantha, osokonezeka, osadziwa za umoyo wao
ndiponso odana ndi anthu. Mosimikiza zonsezi zimapedzeka ku ubongo zomwe zima
gwira mizipe, ndipo munthu kukhala ozelezeka monga odwala (Melancholia) mutuwake.
Akupitiliza Galen kuti munthu otele wa (Dyshmia) amakhala okwiya mwamsanga
(Crasis) ndi ponso ofooka (Chymos).
Robert Borton “kaswili wa” (Anatony of Melancholia) ananena ndi ku ulusa chaka cha
1630, mofotokoza mdondomeko bwino anati (Melancholy) “ndi matenda omwe
amagwira muutu ndi ubongo” nthawi ndi nthawi mo onjezera uwawa ndipo maganizo.
Burton ndiye anadzetsa chibvumbulutso kuti mankhwala amakono akhale odzwa kuti
misaala imabwera bwanji, ndiye ichi ndiye chi*****wa cha ubongo (Depression), kenaka,
uzungulira kwa muutu ndi kukhala wa manyazi, openga, okwiya, osafuna kukomana ndi
mkadzi malo amodzi.
Wina wache kaswiri wa dzina la Freud adalemba mbuuku lache (mourning and
Melancholia) lolembedwa mchaka cha 1917. Anati kulemba Freud (Melancholia), ndi
matenda omwe amapanga munthu ukhala oopa kathu kenache kalikonse monga openga
kapena odabwa ataona kanthu.
Ndiponso (Delusional Depression) yatsimikidzidwa kuti umakanika iwe wekha kukhutira
chili chonse kenaka umakhala ozazuka. Zanveka kuti amisala wa amakhala okwiya,
openga, ozazuka ngati wina wache akunena kapena kulankhula, monga mkadzi akati
tiyeni tikomane za chikwati ama zazuka chi*****wa chila kolako alibe chokumana ndi
mkadzi. Aganizani, taonani zotelezi zingapedzeke kumunthu omwe ali mneneri (Mirza)?
Bwenzi freud ankadziwa akada werenga naeso zauyu Mirza.
Uzelezeka, upenga anthu-anatulukila matendawa kalekale zikwi ndi zikwi zaaka zapitazi.
Oyamba ndi (Philosopher) kenaka asing’anga madotoro. Ufikira lelolino ai zafalitsidwa
pose pose mvipatala ndi madotoro akudziwa bwino zamatenda amisala.
“Ulingana ndi Hikmat ndi Greek mmalamulo awo akuti, matenda awa amabwera
chi*****wa cho chulukira kwa (Black Acidic) mmimba. Kalikonse kamthupi kakagwidwa
ndi Black Acidic kamapangitsa chakudya mmimba ndiposo mmvuche oipa osatuluka,
umapita ku ubongo. Zikatero, zima sanduka ma (Symptoms): odzadzamwa (Anoxia)
chi*****wa matumbo mmimba salibwino ai, chakudya osagaidwa bwino, usegula mmimba
apa ndi apa, kuiwala iwala, kugeya konunkha uchokera mmimba. (kodi mnneri monga
Mirza angakhale ndi umoyo otero?) kalembera akufusa.
(Chionesero chachiyambi cha matenda oopya monga amisalaku ubongo. Olemba Allamba Burhanuddin Nafeesa).
« Zanveka kuti matenda a (Melancholia) ndi zotulukamo, chi*****wa cho lephera upanga
zachikwati ndimkadzi chi*****wa chakuti matendawa amayambira ku (Liver) ndi mmimba.
Koma lero lino, ndi chodziwika kuti ndi matenda amisala monga (Hysteria) kwa azimai.
Chiyambi ndi mmimba ndiye momwe mudzetsa zosezi ukhala ofooka maganizo
(Meloncholia) kwa a zibambo. Chidzindikiro :- odwala openga, maganizo amaganiza
zaiye yekha, kenaka kumati ine ndine ndi chita ichi ndiichi nthawi ndi
nthawi…………………………osafuna kudya, kuvutikila kuchotsa chimbuzi ».
(Makhzan-e-Hikmat, olemba Hakeem Dr. Ghulam Jeelani).
“Kusowewa kupnga chimbudzi, kusegula mmimba (Sailorhea) utuupa mimba
(Borbarygmi), kupsya mmimba, osakoma chakudya, mpweyaoipa uchokera mmimba
upita kumutu, zosezi ziletsa upita ku chimbudzi ndi chakudya, kenaka utentha mamba ndi
thupi, manja ndi miyendo kenaka ku dzidzira kwa thupi kambiri mibiri thupi limafooka,
kambiri maso amawawa, kulema kwazikope, kutentha kwa mutu ndi ubongo, kupweteka
ka mutu zosezi ndi chi*****wa chamatenda akhunyu (Melancholia)”.
(Akseer-e-Azam vol. 1 tsamba 189 olemba Hakeem Muhammad Azam khan).
Mwawerenga zonsezi kulingana ndi nkhani za matenda. Mwapatsidwa mpata nonse kuti
muganize bwino zomwe ozicha kuti ndine mneneri (Mirza) omwe alankhula ndi
Mulungu apezeka ndi matenda monga tanenawa oopsya akhunyu ndi khunyu kumanama
anthu kuti ndine (Messaya) omwe apezeka ndi nthenda ya ( melancholic), anga itandidwe
bwanji kuti ndi mtumiki? Utamusatila mneneri monga uyu kodi ungakhale iweyo
musilam okwana? Musaike chikhulupiliro ndi kukhala okulupilira monga aneneri
onyenga, pokhapo mneneri oma liza iyeyundi mtumiki (Muhammad) S.A.W.
Mtumiki Muhammad (S.A.W) akuti:
“Otsatira aine tanvani, azapezeka aneneri onyenga okwana 30 aliyense mwaiwo onama
amati ndatumidwa ndi Mulungu monga mneneri. Ndi kwainu nonse kudziwa kuti
mneneri onyenga uyu ndani kodi chiwerengero chache ndi chotani? Tsopano tiyeni tione
anzeru zakuya monga akalembera akunena zamatenda a (Melancholia) akhunyu,
kalembela wina monga Hakeem akuti:-
ABU ALI SENA AKUTI:-
“Matenda a (Melancholia) ama mphanga munthu ukhala openga kumalankhula zo
bwebweta bwebweta kumaziganinizira monga ndi munthu weniweni kumaziika
pamtengo wapatali. Akagwidwa ndi khunyu kapena khunyu amanva chidima pamaso
ubongo naonso uma sokonezeka kenaka odwara uja amapenga monga ufuntha chi*****wa
chamdima akagwidwa ndi matenda wa. Kambiri (Liver) mphafa imatentha, amati
matenda a (Hypochonriasis). Chakudya ndi madzi zikalowa mmimba zimakhala zakuda
kapena (blackish) mmimba muja zimatupisa mimba kenaka mphweya umatengedwa
upita ku ubongo, izozo zimapanga (Gaseous Melancholia) ukhala openga nthawi ndi
nthawi”.
(Canon in Medicine, Fun-E-Awwal book ya 3, Abu Ali Sena).
Kachilitsidwe: ndikofunikira munthu odwala (Melancholia) akhale otangwanika ndi
zinchito izi ndi izi ndi kuti mtima wake upuume bwino ndiposo akhale pafupi ndi anthu
omwe azamnama kuti ndinu nokha ndinu nokha kuti iye yo odwala uja azikhala
okondwera kenaka usakuikamozako ndiviinyu (Wine) kuti odwala uja akhale osangalala
ataledzera pangono”.
(Canon in Medicine olembe ndi Aviecnia).
Dziwa: Mirza Ghulam Ahmad Qadiani anali kumwa mowa (Wine) ndi mapilisi
oledzeletsa (Opium) chi*****wa cha matenda ache.
“(Melancholia) ayandi matenda omwe amasokoneza maganizo abwino kukhala openga
ngati wamisala chi*****wa samakhala munthu okwana ai”.
Kambirimbiri odwala amakhala munthu okamba kamba zinthu zopanda pache kenaka ndi
kumalodzela zomwe zolota kuti zaku tsogolo zikhala motele motele zabodza basi.
Kenaka imafika nthawi yakuti amanena kuti iyeyo ndimgero”.
(Guide to the Aetiology ndi chiyambi chamatenda ya Melancholia olemba ndi Allama Burhanuddin Nafees).
Zosezi zamatenda awa ndi zotulukamo zimadza momwe takambila pachiyambipo
chi*****wa cha umoyo wa munthu. Mfano, ngati munthu wa chikhulupiliro omwe
wamisala angaziche iyo mneneri ndi kuonetsa zodabwitsa (Miracles) ofuntha kuma
lankhula mau aulariki ndi chipulumutso kuanthu, zitheka bwanji munthu openga
oteroyu?”
(Akseer-e-Azam vol. 1 tsama la 188 olemba ndi Muhammad Azam Khan).
“Odzicha iyeyo mneneri, ngati nizoona bwanji adwara matenda a misala (Hysteria)
monga kupenga (Melancholia) kapena khunyu (Epilepsy), ichi ndiye chidzindikiro
chakuti iyeyu sanga khale mneneri ai, chi*****wa izi zonse zimampangisa iyeyo mneneri
onyenga ukhala ndithu onyenga kapena onama alibe chiyambi ai”.
(Slemba ndi Dr. shahanawaz Qadiani mu Magazine ya onani chipembezo, Qadiani tsiku August 1926 A.D).
Mirza Qadiani ndi mowa + uledzera (Drug ndiye mkhlidwe wache.
“(Opium) zidonge ndi mapilisi oledzeletsa zimapendzeka kumunthu odwara misala
(Hazrat Maseeh Mirza Ghulam Ahmad Qadiani) amanena kuti mapilisi oledzeletsa kwa a
dotoro ake, (Opium) ndi amodzi omwe andi chiritsa ine. Chomwechi (Opium) pamodzi
ndi mankhwara ena amachilitsa ndipo uledzera nakoso ndichimodzimodzi nazonso zima
chilitsa. Chi*****wa wina wache mwaife nthawi ina ana mwapo (Opium).
“Hazrat Maseeh Mawood onyenga mneneri Mirza Ghulam Ahmad Qadiani adalonjedza
kuti mankhwara (Tiryaq –E-Llahi kuti (Opium) ndi mankhwala ochokera kwa Mulungu.
Kambiri aya mankhwala ana mpatsa kumwa uyu mneneri onyenga Hazrat Khalifa
oyamba – Hakeem Noorud Din olemba Hazrat (Mirza Qadiani) anali kumwa mneneri
onama uyu miyezi 6, nayenso akagwidwa ndi khunyu naenso anali kumwa (Opium)”.
(Article olemba ndi Mian Mahmood Ahmad khalifa Qadiani mbuukula Akber Al Fazal, Qadian vol. 17 no. 6 pa 19th July 1929).
Vinyu (Tonic Wine):-
“Kwa okondedwa mbale Muhammad Hussein Sahib Mulungu akudalitse. Assalam-oalaikum
Chiyambi iwe mohammad watumidwa lero. Zipangizo ziri tayari. Funafuna zipangizo
zako botoro limodzi la vinyu (Tonic Wine) uchokera musitolo La Plommer koma ndifuna
botolo la vinyu (Tonic Wine) sunga mmutu wako. Zose ziri bwino.
(osaina: Mirza Ghulam Ahmad Qadiani).
(Makalata a Imam kwa P. S. Olemba Mirza Ghulam Ahmad Qadiani upita kwa Hakem Mohammad Husain Qadiani, mwini wa chipatala Rafiq-us-sahat Lahore Pakistan).
Choonadi cha vinyu (Tonic Wine) amaguula kusitoro la Plommer boma la Lahore
Pakistan umboni opitira mwa Dr. Aziz Ahmad anati polemba:-
Ndalamulidwa kuti ndizigula mowa uyu wa vinyu (Tonic Wine) mustitoro la Plommer,
adayankha nati:
“Vinyu (Tonic Wine) ndi mowa oledzeletsa oopsya omwe umagulidwa ndi maiko akunja monga ku (U.K) muma botoro otsekedwa bwino bwino. Mtengo wache ndi R.S. Annas 8
(1-09-1933)”.
(Sauda-e-Mirza tsamba 39 olemba Hakeem Muhammad Ali, mkulu wasukulu ya Tibbiya
boma la Amratsar).
Taonani pangwe ngwengwe mneneri onyenga zomwe za turukamo kuti Mirza Ghulam
Ahmad Qadiani saku kwana ai kukhala mneneri, kapena kukhala uja olengezedwa monga
(Mahdi) mwina monga mphulumutsi ai, mpulumutsi sanga khale ndi matenda a khunyu,
misala, ozelezeka sizingatheke oteleyo woledzera alankhulane ndi Mulungu ai. Kenaka
kwaturuka onyengayu akumwa (Opium) ndi mowa ai sakwana pa uneneri. Tiyeni
timpemphe Mulungu ati onetse njira ya chilungamo ndi kudzindikira kuti tionetsetse
aupandu awa a Qadiani naonso atsatire choonadi cha chipembezo cha mtumiki wathu
omalidza Muhammad (S.A.W). Zikanga kuti atsatire chilungama cha choonadi ndi
kumatsatira anthu a chinyulunyulu, akhunyu, amisala (Melancholiac Prophet) naonso
azakhala chimodzi modzi monga mneneri wao onyenga ndiposo chipembezo chaocho
chikhala chonyenga dziwani kuti moto wa Jahena udikhira anthu onyenga.
END
Translated from English to Nyanja by :
OLEMBA NDINE SHEIKH ASSADULLAH MWALE
MUFTI OF ZAMBIA
P. O. BOX FW 306
LUSAKA – ZAMBIA
CELL: +260 97 7493870
EMAIL: assadullahmwale@yahoo.com
Anti Ahmadiyya Movement in Islam
Dr Syed Rashid Ali
P.O.Box 11560 Dibba Al Fujairah
United Arab Emirates.
E-mail: rasyed@emirates.net.ae / alhafeez.org/rashid