عرض المقال :Qadiani Conspiracy Exposed
  الصفحة الرئيسية » مـقـالات الموقـــع » كشف البلية بفضح الأحمدية » Non - Arabic Articles » Nayanga/Chichewa

اسم المقال : Qadiani Conspiracy Exposed
كاتب المقال: webmaster

Muhibban-e-Mustafaصلى الله عليه وسلم

Ahmadiyya Awareness Campaign

Praise be to Allah, One and only. His Love and Blessings may shower on Seydna Muhammadصلى الله عليه وسلم after whom there is no prophet and upon His Pious Family and Respected Companions

CHINYENGO CHA QADIANI CHA SOKOLOKA

Qadiani anafuna kuti apange Vatican-style ikhazikidwe mu Pakistani.

(India akhazi kitsa guulu la chiwembu la Qadiani komweko).

25th December 1997 mu weekly Takbeer,

olemba ndi Farooq Adil.

Iyi nkani ndi yakale kale ku Pakistan, oyamba myezi yakale chaka cha 1947 pomwe Pakistan akadalibe kukhala mchiwerengero cha dziko. Achipembezo a mtundu wa Punjab adatuma kalata ku dziko la Britain kuti asa loledwe kuti nao ndi amodzi a guulu la Aslam. Chi*****wa angakhale aliku India koma siali Aslam.

Omwe odziwa movement ya Pakistan oyamba nthawi ya Khalifa wa chiwili uyu wa Mirza Ghulam Ahmed Qadiani. Cho dabwitsa ndi ichi kuti msogoleri wa ma Hindu ndiye omwe ada lesa kuti Qadiani asaloledwe kuti ndi Aslam. Koma a Britain ada vomera pemdo lolesa Qadiani Aslam Nthawi iyo adali ochepekela chiwerengero cha51% ku Gurdaspur, Ferozpur Andi mu Amristar.

Anaphedwa ambiri Aslam mu Punjab omwe ambiri anathawira ku kashimir. Mpakana lelo mabvuto akali kupitilila komweko ku Kashmir Sir. Zafarulla Khan ana wa sonkhanisa pa ma jiga amaiko awiri. Izi zida chitika nthani ya Sir. Zafarulla Khan omwe adalengeza ku ziko la Britan.

Izi zanali panthawi ya musogoleri wa chiwiri wa Ahmadiya Jamati, Mirza Basheeruddin Mahmood ndi kalembela Allama Iqbal izi zodziwika kuti Kashmir committee chaka cha 1931.

Gulu la Qadian ndilotismiki za kuti Mirza Ghulam Ahmed Qadiani sanali Mtumiki Chabe Komaso Messiah Mukhulupilira kuti hazarat Eisa (Yesu) (A.S) manda ake ndithu ali ku Kashmir. Kotero Kashmir ndiye malo a gulu la Qadiani oyera mchipembezo chao.

Izi zida choka poyera nthawi Mirza Ghulam Ahmed Qanani ata mwalira, pomwe uyu wa chiwiri Hakeem Nuruddin omwe wa chiwiri mu Qadiani kapena Ahamadiya movement. Ena akuti manda a Yesu ali ku Srinagar.

Panthawi ya chaka 1931 ndiye pomwe udani ndi gulu la Qadiani una kula pakati ba anthu. Pomwe gulu la Qadiani linayamba kashmir Chalo Movement usogolela msokonezo waukulu limodzi ndi Allama Iqbal. Kumbukila kale gulu la Qadiani anali ku zicha naoso Asilam.

Chi*****wa chaichi gulu lu Qadiani linapemphedwa kuti linene poyela kuti ndi gulu la Qadiani kenaka azapatsidwa malo ao ao pakati pa Pakistan, Sialkot ndi Shakergarh-Kashmir.

Chaka cha 1947 msokonezo una yamba pakat, pao ndi gulu la Sikh. Chi*****wa gulu la Sikh silinali kudziwa Muslam weni weni ndani pakat pa Qadiani ndi Asilam. Ena anapita Gurdaspur, Ferozpur ndi Amritsar.

Gulu la Qadiani linalephela ukhazikisa Vetican-style city. Koma boma la India lina funisia kuti gulu la Qadiani likhale ndi likuulu lake ku East Punjab.

Koma Independence Pakistan sili nalole Qararbad –e-Maqaased kuti likhazi kidwe.

Muphwa wa Sir. Zafarulla Khan, Mr. Zafar Chaudhary Ana sogolela Upitiliza Pomwe Ana siya Mirza Tahir Ahamd Gulu La Ahmandiyya Jamaat uyu anali wa mkulu nduna ya Sindh Mr. Kanwar Idrees, Pamodzi Ndi Pakistan Human Rights Commission Wa Asma Iahangir Mwamuna weke anali Qadiani.

Ndi chodziwika kuti boma la Pakistan la lengeza kuti Qadiani ali ndi camp la terrorist mudzikola India East Puntab. Ama nama upyolera mu Jamaat Ahamadiyya upita ku Qadiani./ kutalika kwake uchoka ku Shakergarh ndi Qadiani 20-25 miles.

Tikaonetsesa, Shakergarh ndi likulu mziko la India kenaka Tilford ndi likuulu mziko la Britain UK Momwe Ahamadiyya ili Headquarters ya upandu la terrorist.

Koma uchokera chaka 1974 lamulo lina khazi kidwa kuti Qadiani si Asilam ai. Inali nthawi ya Gen. Zia ulhaq.

Chaka cha 1984 Mirza Tahir Ahmad ana thawira ku London, Chomwe cho upandu ndi terrorism pakati pa India-Pakistan kwalima ndi Britain. Qadian ina yamba mu Pakistan chaka cha 1953.

Nthawi ya Zulfiqar Ali Bhutto, uyu Mirza Tahir Ahmad anali pafupi pomwe anali kuyamba chipani cha Peoples Party. Ndithu anali pafupifupi usonyeza kuti adali limodzi mugulu la Qadiani.

Zaka zapita kumbuyo 1970 mpaka 1980 anka funakuti akhazi kise Vertican –style ya Qadiani monga a Christo.

 

 

CHENJEZO

1.      Uyu Mirza Tahir akapita ku London uchoka ku India achenjere naye chi*****wa cha terrorist.

 

2.      Chipani cha people’s party maka maka Khalid Kharral omwe anali ku India zaka ziwiri (2 years) nayeso ndi wa upandu terror.

 

3.      Chenjezo lina Qadiani azi yense asapasidwe Asylum ya ndale ku Britain, Europe, America ndi ku far East, pamodzi ndi ma Diplomats.

 

4.      Omwe ogwira chito ku Human –Rights agulu la Qadiani monga Zafar Chaudhry asaloledwe-Chi*****wa ndi aupanmdu. Malile a Sialkot, Shakergarah ndi ina mipaka sungani bwino chi*****wa chaupandu.      

 

Anti Ahmadiyya Movement in Islam

Dr Syed Rashid Ali

Box 11560 Dibba Al Fujairah

United Arab Emirates

http://.alhafeez.org/rashid.

E-mail: rasyed@emirates.net.ae.

 

اضيف بواسطة :   admin       رتبته (   الادارة )
التقييم: 0 /5 ( 0 صوت )

تاريخ الاضافة: 26-11-2009

الزوار: 2314


جديد قسم مـقـالات الموقـــع
القائمة الرئيسية
البحث
البحث في
القائمة البريدية

اشتراك

الغاء الاشتراك